Add parallel Print Page Options

44 Iye anawawuza kuti, “Izi ndi zimene ndinakuwuzani pamene ndinali nanu: chilichonse chiyenera kukwaniritsidwa chimene chinalembedwa cha Ine mʼbuku la Malamulo a Mose, Aneneri ndi Masalimo.”

Read full chapter

45 Kenaka anawatsekula maganizo kuti azindikire Malemba.

Read full chapter