Matthew 5:47-48
Christian Standard Bible
47 And if you greet only your brothers and sisters, what are you doing out of the ordinary?[a](A) Don’t even the Gentiles[b] do the same? 48 Be perfect,(B) therefore, as your heavenly Father is perfect.
Read full chapter
Mateyu 5:47-48
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
47 Ndipo ngati inu mupatsa moni abale anu okhaokha mukuchita chiyani choposa ena? Kodi ngakhale akunja sachita chimodzimodzi? 48 Nʼchifukwa chake, inu khalani angwiro monga Atate anu akumwamba ali wangwiro.”
Read full chapterThe Christian Standard Bible. Copyright © 2017 by Holman Bible Publishers. Used by permission. Christian Standard Bible®, and CSB® are federally registered trademarks of Holman Bible Publishers, all rights reserved.
The Word of God in Contemporary Chichewa Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.® Used by permission of Biblica, Inc.® All rights reserved worldwide. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.® Kugwiritsa ntchito mwachilolezo. Umwini ndi otetezedwa pa dziko lonse.