Add parallel Print Page Options

Yesu Adzipempherera Yekha

17 Yesu atatha kunena izi, anayangʼana kumwamba ndipo anapemphera:

“Atate, nthawi yafika. Lemekezani Mwana wanu, kuti Mwana wanuyo akulemekezeni Inu.

Read full chapter