Font Size
2 Akorinto 3:1
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
2 Akorinto 3:1
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Akhristu ndi Kalata Yochokera kwa Khristu
3 Kodi tayambanso kudzichitira umboni tokha? Kapena kodi ifenso tikufuna makalata otivomereza kwa inu, kapena ochokera kwa inu monga anthu ena?
Read full chapter
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero (CCL)
The Word of God in Contemporary Chichewa Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.® Used by permission of Biblica, Inc.® All rights reserved worldwide. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.® Kugwiritsa ntchito mwachilolezo. Umwini ndi otetezedwa pa dziko lonse.